2 Mbiri 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapita kumalo okwezeka ku Gibiyoni.+ Anapita kumeneko chifukwa nʼkumene kunali chihema chokumanako cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki wa Yehova anapanga mʼchipululu.
3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapita kumalo okwezeka ku Gibiyoni.+ Anapita kumeneko chifukwa nʼkumene kunali chihema chokumanako cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki wa Yehova anapanga mʼchipululu.