2 Mbiri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Davide anali atachotsa Likasa la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu+ nʼkukaliika pamalo amene anakonza. Iye anali atamanga tenti ya Likasalo ku Yerusalemu.+
4 Koma Davide anali atachotsa Likasa la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu+ nʼkukaliika pamalo amene anakonza. Iye anali atamanga tenti ya Likasalo ku Yerusalemu.+