2 Mbiri 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Guwa lansembe lakopa*+ limene Bezaleli+ mwana wa Uri mwana wa Hura anapanga, anali ataliika patsogolo pa chihema chopatulika cha Yehova. Ndipo Solomo ndi mpingowo ankapemphera patsogolo pa guwalo.
5 Guwa lansembe lakopa*+ limene Bezaleli+ mwana wa Uri mwana wa Hura anapanga, anali ataliika patsogolo pa chihema chopatulika cha Yehova. Ndipo Solomo ndi mpingowo ankapemphera patsogolo pa guwalo.