2 Mbiri 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Solomo anapereka nsembe zopsereza 1,000 pamaso pa Yehova, paguwa lansembe lakopalo+ limene linali kuchihema chokumanako.
6 Kenako Solomo anapereka nsembe zopsereza 1,000 pamaso pa Yehova, paguwa lansembe lakopalo+ limene linali kuchihema chokumanako.