2 Mbiri 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usiku wa tsiku limenelo, Mulungu anaonekera kwa Solomo nʼkumuuza kuti: “Pempha chimene ukufuna ndikupatse.”+
7 Usiku wa tsiku limenelo, Mulungu anaonekera kwa Solomo nʼkumuuza kuti: “Pempha chimene ukufuna ndikupatse.”+