2 Mbiri 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Solomo atamva zimenezi anauza Mulungu kuti: “Inu mwasonyeza kwambiri chikondi chokhulupirika kwa mtumiki wanu Davide+ bambo anga ndipo mwandiika kukhala mfumu mʼmalo mwake.+
8 Solomo atamva zimenezi anauza Mulungu kuti: “Inu mwasonyeza kwambiri chikondi chokhulupirika kwa mtumiki wanu Davide+ bambo anga ndipo mwandiika kukhala mfumu mʼmalo mwake.+