2 Mbiri 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ndikupatsa nzeru ndi luso lodziwa zinthu. Ndikupatsanso katundu, chuma ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhaleko ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+
12 ndikupatsa nzeru ndi luso lodziwa zinthu. Ndikupatsanso katundu, chuma ndi ulemu zochuluka kwambiri kuposa zimene anali nazo mafumu amene anakhalako iwe usanakhaleko ndiponso zoposa zimene aliyense wobwera pambuyo pako adzakhale nazo.”+