2 Mbiri 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Solomo anasonkhanitsa magaleta ndi mahatchi,* moti anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi* 12,000.+ Zonsezi ankazisunga mʼmizinda yosungiramo magaleta+ ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+
14 Solomo anasonkhanitsa magaleta ndi mahatchi,* moti anakhala ndi magaleta 1,400 ndi mahatchi* 12,000.+ Zonsezi ankazisunga mʼmizinda yosungiramo magaleta+ ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+