2 Mbiri 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva ndi golide akhale wambiri ngati miyala+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ambiri ngati mitengo yamkuyu ya ku Sefela.+
15 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva ndi golide akhale wambiri ngati miyala+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ambiri ngati mitengo yamkuyu ya ku Sefela.+