2 Mbiri 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Solomo analamula kuti amange nyumba ya dzina la Yehova+ ndi nyumba yachifumu ya Solomoyo.+