2 Mbiri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso Solomo anatumiza uthenga kwa Hiramu+ mfumu ya Turo, wakuti: “Mundichitire zomwe munachitira bambo anga Davide. Paja munawatumizira mitengo ya mkungudza kuti amangire nyumba* yawo yokhalamo.+
3 Komanso Solomo anatumiza uthenga kwa Hiramu+ mfumu ya Turo, wakuti: “Mundichitire zomwe munachitira bambo anga Davide. Paja munawatumizira mitengo ya mkungudza kuti amangire nyumba* yawo yokhalamo.+