2 Mbiri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ineyo ndipereka chakudya cha antchito anu+ odula mitengo. Ndipereka tirigu wokwanira makori* 20,000, balere makori 20,000, vinyo mitsuko* 20,000 ndi mafuta mitsuko 20,000.”
10 Ineyo ndipereka chakudya cha antchito anu+ odula mitengo. Ndipereka tirigu wokwanira makori* 20,000, balere makori 20,000, vinyo mitsuko* 20,000 ndi mafuta mitsuko 20,000.”