2 Mbiri 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Hiramu anati: “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa wapereka kwa Mfumu Davide mwana wanzeru,+ wozindikira komanso womvetsa zinthu+ yemwe amange nyumba ya Yehova komanso ya ufumu wake.
12 Kenako Hiramu anati: “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa wapereka kwa Mfumu Davide mwana wanzeru,+ wozindikira komanso womvetsa zinthu+ yemwe amange nyumba ya Yehova komanso ya ufumu wake.