2 Mbiri 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ife tidula mitengo yambiri mmene inu mukufunira kuchokera ku Lebanoni,+ ndipo tiziimanga mʼmaphaka oti aziyandama nʼkuitumiza panyanja kukafika ku Yopa.+ Inu muzikaitengera kumeneko nʼkupita nayo ku Yerusalemu.”+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 16
16 Ife tidula mitengo yambiri mmene inu mukufunira kuchokera ku Lebanoni,+ ndipo tiziimanga mʼmaphaka oti aziyandama nʼkuitumiza panyanja kukafika ku Yopa.+ Inu muzikaitengera kumeneko nʼkupita nayo ku Yerusalemu.”+