2 Mbiri 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Solomo anawerenga amuna onse amene anali alendo mʼdziko la Isiraeli+ ngati mmene Davide bambo ake anachitira.+ Ndipo panapezeka amuna okwana 153,600.
17 Kenako Solomo anawerenga amuna onse amene anali alendo mʼdziko la Isiraeli+ ngati mmene Davide bambo ake anachitira.+ Ndipo panapezeka amuna okwana 153,600.