2 Mbiri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho iye anasankhapo amuna 80,000 kuti akhale osema miyala+ kumapiri, amuna 70,000 kuti azigwira ntchito zina* komanso amuna 3,600 kuti akhale oyangʼanira anthuwo pa ntchito yawo.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:18 Nsanja ya Olonda,12/1/2005, tsa. 19
18 Choncho iye anasankhapo amuna 80,000 kuti akhale osema miyala+ kumapiri, amuna 70,000 kuti azigwira ntchito zina* komanso amuna 3,600 kuti akhale oyangʼanira anthuwo pa ntchito yawo.+