2 Mbiri 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Golide wa misomali yake anali wolemera masekeli* 50 ndipo zipinda zake zapadenga anazikuta ndi golide.
9 Golide wa misomali yake anali wolemera masekeli* 50 ndipo zipinda zake zapadenga anazikuta ndi golide.