2 Mbiri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mʼchipinda cha Malo Oyera Koposa anapangamo zifaniziro ziwiri za akerubi nʼkuzikuta ndi golide.+