2 Mbiri 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mapiko otambasula a akerubiwo anali aatali mikono 20. Akerubiwo anali ataimirira ndipo nkhope zawo zinayangʼana mkati.*
13 Mapiko otambasula a akerubiwo anali aatali mikono 20. Akerubiwo anali ataimirira ndipo nkhope zawo zinayangʼana mkati.*