2 Mbiri 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuchindikala kwa thankiyo kunali chikhatho* chimodzi. Milomo yake inali ngati kukamwa kwa mphika kapena ngati maluwa. Muthankiyo munkalowa madzi okwana mitsuko* 3,000. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:5 Nsanja ya Olonda,2/1/2008, tsa. 1512/1/2005, tsa. 19
5 Kuchindikala kwa thankiyo kunali chikhatho* chimodzi. Milomo yake inali ngati kukamwa kwa mphika kapena ngati maluwa. Muthankiyo munkalowa madzi okwana mitsuko* 3,000.