2 Mbiri 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anapanganso mabeseni 10 ndipo anaika mabeseni 5 kumanja, mabeseni 5 kumanzere.+ Mʼmabeseniwo ankatsukiramo zinthu zimene ankagwiritsa ntchito popereka nsembe yopsereza.+ Koma ansembe ankasamba madzi a muthanki ija.+
6 Iye anapanganso mabeseni 10 ndipo anaika mabeseni 5 kumanja, mabeseni 5 kumanzere.+ Mʼmabeseniwo ankatsukiramo zinthu zimene ankagwiritsa ntchito popereka nsembe yopsereza.+ Koma ansembe ankasamba madzi a muthanki ija.+