2 Mbiri 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anapanga zoikapo nyale 10 zagolide+ mogwirizana ndi zomwe anauzidwa+ nʼkuziika mʼkachisi. Anaika 5 kumanja, 5 kumanzere.+
7 Kenako anapanga zoikapo nyale 10 zagolide+ mogwirizana ndi zomwe anauzidwa+ nʼkuziika mʼkachisi. Anaika 5 kumanja, 5 kumanzere.+