2 Mbiri 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anapanganso matebulo 10 nʼkuwaika mʼkachisi. Anaika 5 kumanja, 5 kumanzere+ ndipo anapanganso mbale zolowa 100 zagolide.
8 Iye anapanganso matebulo 10 nʼkuwaika mʼkachisi. Anaika 5 kumanja, 5 kumanzere+ ndipo anapanganso mbale zolowa 100 zagolide.