2 Mbiri 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anapanga bwalo+ la ansembe+ ndi bwalo lalikulu* komanso zitseko za bwalo lalikululo.+ Zitsekozo anazikuta ndi kopa.
9 Ndiyeno anapanga bwalo+ la ansembe+ ndi bwalo lalikulu* komanso zitseko za bwalo lalikululo.+ Zitsekozo anazikuta ndi kopa.