2 Mbiri 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Hiramu anapanganso ndowa, mafosholo ndi mbale zolowa.+ Choncho iye anamaliza ntchito imene ankagwirira Mfumu Solomo panyumba ya Mulungu woona.+
11 Hiramu anapanganso ndowa, mafosholo ndi mbale zolowa.+ Choncho iye anamaliza ntchito imene ankagwirira Mfumu Solomo panyumba ya Mulungu woona.+