2 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawi imeneyo Solomo anasonkhanitsa akulu a Isiraeli, atsogoleri onse a mafuko ndi atsogoleri a nyumba za makolo a Aisiraeli. Anabwera ku Yerusalemu kuti akatenge likasa la pangano la Yehova ku Mzinda wa Davide,+ komwe ndi ku Ziyoni.+
2 Pa nthawi imeneyo Solomo anasonkhanitsa akulu a Isiraeli, atsogoleri onse a mafuko ndi atsogoleri a nyumba za makolo a Aisiraeli. Anabwera ku Yerusalemu kuti akatenge likasa la pangano la Yehova ku Mzinda wa Davide,+ komwe ndi ku Ziyoni.+