2 Mbiri 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo ananyamula Likasa, chihema chokumanako+ ndiponso ziwiya zonse zopatulika zimene zinali mʼchihemacho. Ansembe ndi Alevi* anabweretsa zinthuzi.
5 Iwo ananyamula Likasa, chihema chokumanako+ ndiponso ziwiya zonse zopatulika zimene zinali mʼchihemacho. Ansembe ndi Alevi* anabweretsa zinthuzi.