2 Mbiri 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova pamalo ake, kuchipinda chamkati cha nyumbayo, chomwe ndi Malo Oyera Koposa, ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+
7 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova pamalo ake, kuchipinda chamkati cha nyumbayo, chomwe ndi Malo Oyera Koposa, ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+