-
2 Mbiri 5:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mitengo yonyamulirayo inali yaitali moti nsonga zake zinkaonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinkaonekera panja. Mitengoyo idakali pomwepo mpaka lero.
-