2 Mbiri 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mu Likasalo munalibe chinthu china chilichonse kupatulapo miyala iwiri yosema imene Mose anaikamo ku Horebe.+ Anaiikamo pa nthawi imene Yehova anachita pangano+ ndi Aisiraeli, pamene ankachoka mʼdziko la Iguputo.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:10 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 31
10 Mu Likasalo munalibe chinthu china chilichonse kupatulapo miyala iwiri yosema imene Mose anaikamo ku Horebe.+ Anaiikamo pa nthawi imene Yehova anachita pangano+ ndi Aisiraeli, pamene ankachoka mʼdziko la Iguputo.+