2 Mbiri 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Kuyambira tsiku limene ndinatulutsa anthu anga mʼdziko la Iguputo, sindinasankhe mzinda mʼmafuko onse a Isiraeli womangako nyumba ya dzina langa kuti likhale kumeneko.+ Ndipo sindinasankhe munthu woti alamulire anthu anga Aisiraeli.
5 ‘Kuyambira tsiku limene ndinatulutsa anthu anga mʼdziko la Iguputo, sindinasankhe mzinda mʼmafuko onse a Isiraeli womangako nyumba ya dzina langa kuti likhale kumeneko.+ Ndipo sindinasankhe munthu woti alamulire anthu anga Aisiraeli.