2 Mbiri 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wakwaniritsa zimene analonjeza, chifukwa ndalowa mʼmalo mwa bambo anga Davide ndipo ndakhala pampando wachifumu wa Isiraeli,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza.+ Komanso ndamanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.
10 Yehova wakwaniritsa zimene analonjeza, chifukwa ndalowa mʼmalo mwa bambo anga Davide ndipo ndakhala pampando wachifumu wa Isiraeli,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analonjeza.+ Komanso ndamanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wa Isiraeli.