2 Mbiri 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Maso anu akhale akuyangʼana nyumba ino masana komanso usiku. Akhale akuyangʼana malo amene munanena kuti dzina lanu lidzakhala kumeneko,+ kuti mumvetsere pemphero limene mtumiki wanu angapemphere atayangʼana kumalo ano.
20 Maso anu akhale akuyangʼana nyumba ino masana komanso usiku. Akhale akuyangʼana malo amene munanena kuti dzina lanu lidzakhala kumeneko,+ kuti mumvetsere pemphero limene mtumiki wanu angapemphere atayangʼana kumalo ano.