2 Mbiri 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mumve pemphero la mtumiki wanu lopempha thandizo komanso la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayangʼana malo ano.+ Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ mumve nʼkukhululuka.+
21 Mumve pemphero la mtumiki wanu lopempha thandizo komanso la anthu anu Aisiraeli, limene angapemphere atayangʼana malo ano.+ Inuyo mumve muli kumalo anu okhala, kumwamba,+ mumve nʼkukhululuka.+