2 Mbiri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu posonyeza amene ali wolakwa pobwezera wolakwayo mogwirizana ndi zochita zake+ komanso musonyeze amene ali wosalakwa nʼkumupatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+
23 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu posonyeza amene ali wolakwa pobwezera wolakwayo mogwirizana ndi zochita zake+ komanso musonyeze amene ali wosalakwa nʼkumupatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+