2 Mbiri 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mʼdzikomo mukagwa njala,+ mliri,+ mphepo yotentha yowononga mbewu, matenda ambewu a chuku,+ dzombe,+ ziwala zowononga, mliri wamtundu uliwonse, nthenda yamtundu uliwonse komanso adani awo akawaukira+ mʼmizinda yawo,+
28 Mʼdzikomo mukagwa njala,+ mliri,+ mphepo yotentha yowononga mbewu, matenda ambewu a chuku,+ dzombe,+ ziwala zowononga, mliri wamtundu uliwonse, nthenda yamtundu uliwonse komanso adani awo akawaukira+ mʼmizinda yawo,+