-
2 Mbiri 6:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Muchite zimenezi kuti iwo azikuopani poyenda mʼnjira zanu masiku onse amene angakhale ndi moyo mʼdziko limene munapatsa makolo athu.
-