2 Mbiri 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 ndiyeno iwo nʼkuzindikira kulakwa kwawo mʼdziko limene anawatengeralo nʼkulapa, ndiponso akapempha chifundo kwa inu mʼdziko la adani awowo nʼkunena kuti, ‘Tachimwa, talakwitsa ndiponso tachita zinthu zoipa,’+
37 ndiyeno iwo nʼkuzindikira kulakwa kwawo mʼdziko limene anawatengeralo nʼkulapa, ndiponso akapempha chifundo kwa inu mʼdziko la adani awowo nʼkunena kuti, ‘Tachimwa, talakwitsa ndiponso tachita zinthu zoipa,’+