38 nʼkubwerera kwa inu ndi mtima wawo wonse+ ndi moyo wawo wonse, mʼdziko limene anapita nawo atawagwira,+ ndiponso akapemphera kwa inu atayangʼana kudziko lawo limene munapatsa makolo awo, mzinda umene mwasankha+ komanso nyumba ya dzina lanu imene ndamanga,