2 Mbiri 6:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone ndipo makutu anu akhale tcheru kumvetsera pemphero loperekedwa pamalo ano.+
40 Tsopano Mulungu wanga, chonde, maso anu aone ndipo makutu anu akhale tcheru kumvetsera pemphero loperekedwa pamalo ano.+