2 Mbiri 6:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Inu Yehova Mulungu nyamukani mulowe mʼmalo oti mupumeko,+ inuyo komanso Likasa limene mumasonyezera mphamvu zanu. Ansembe anu, inu Yehova Mulungu, avale chipulumutso ndipo okhulupirika anu asangalale chifukwa cha ubwino wanu.+
41 Inu Yehova Mulungu nyamukani mulowe mʼmalo oti mupumeko,+ inuyo komanso Likasa limene mumasonyezera mphamvu zanu. Ansembe anu, inu Yehova Mulungu, avale chipulumutso ndipo okhulupirika anu asangalale chifukwa cha ubwino wanu.+