2 Mbiri 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ansembe sanathe kulowa mʼnyumba ya Yehova chifukwa ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehova.+