2 Mbiri 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo Solomo anachita chikondwerero masiku 7+ pamodzi ndi Aisiraeli onse. Linali gulu lalikulu la anthu amene anachokera kumadera osiyanasiyana, kuyambira ku Lebo-hamati* nʼkutsetsereka mpaka kukafika kuchigwa* cha Iguputo.+
8 Pa nthawi imeneyo Solomo anachita chikondwerero masiku 7+ pamodzi ndi Aisiraeli onse. Linali gulu lalikulu la anthu amene anachokera kumadera osiyanasiyana, kuyambira ku Lebo-hamati* nʼkutsetsereka mpaka kukafika kuchigwa* cha Iguputo.+