2 Mbiri 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma pa tsiku la 8* anachita msonkhano wapadera+ chifukwa kwa masiku 7 anatsegulira guwa lansembe ndipo kwa masiku 7 ena anachita chikondwerero.
9 Koma pa tsiku la 8* anachita msonkhano wapadera+ chifukwa kwa masiku 7 anatsegulira guwa lansembe ndipo kwa masiku 7 ena anachita chikondwerero.