2 Mbiri 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Yehova anaonekera kwa Solomo+ usiku nʼkumuuza kuti: “Ndamva pemphero lako ndipo ndasankha malo ano kukhala nyumba yanga yoperekeramo nsembe.+
12 Kenako Yehova anaonekera kwa Solomo+ usiku nʼkumuuza kuti: “Ndamva pemphero lako ndipo ndasankha malo ano kukhala nyumba yanga yoperekeramo nsembe.+