2 Mbiri 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 anthu anga otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa,+ kupemphera, kundifunafuna komanso kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba nʼkuwakhululukira tchimo lawo ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:14 Galamukani!,2/8/1994, tsa. 12
14 anthu anga otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa,+ kupemphera, kundifunafuna komanso kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba nʼkuwakhululukira tchimo lawo ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+