2 Mbiri 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndasankha ndi kuyeretsa nyumbayi kuti dzina langa likhale pamenepa mpaka kalekale+ ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala pamenepa nthawi zonse.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:16 Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu,3/2023, tsa. 6
16 Ndasankha ndi kuyeretsa nyumbayi kuti dzina langa likhale pamenepa mpaka kalekale+ ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala pamenepa nthawi zonse.+