2 Mbiri 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iweyo ukayenda mʼnjira zanga ngati mmene bambo ako Davide anachitira, pochita zonse zimene ndakulamula ndiponso ukamamvera malangizo anga ndi ziweruzo zanga,+
17 Iweyo ukayenda mʼnjira zanga ngati mmene bambo ako Davide anachitira, pochita zonse zimene ndakulamula ndiponso ukamamvera malangizo anga ndi ziweruzo zanga,+