2 Mbiri 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma inuyo mukadzatembenuka nʼkusiya kutsatira malamulo anga amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina ndi kuigwadira,+
19 Koma inuyo mukadzatembenuka nʼkusiya kutsatira malamulo anga amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina ndi kuigwadira,+