2 Mbiri 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo nyumbayi idzakhala bwinja. Aliyense wodutsa pafupi adzaiyangʼana modabwa,+ ndipo adzati, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova anachitira zimenezi dzikoli komanso nyumbayi?’+
21 Ndipo nyumbayi idzakhala bwinja. Aliyense wodutsa pafupi adzaiyangʼana modabwa,+ ndipo adzati, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova anachitira zimenezi dzikoli komanso nyumbayi?’+